title

Radio Maria Malawi

Radio Maria Malawi

1
Followers
0
Plays
Radio Maria Malawi
Radio Maria Malawi

Radio Maria Malawi

Radio Maria Malawi

1
Followers
0
Plays
OVERVIEWEPISODESYOU MAY ALSO LIKE

Details

About Us

Radio Maria Malawi

Latest Episodes

Kodi Episikopi amasankhidwa bwanji?

Kodi Apapa amasankha bwanji Episikopi?

33 MIN2018 MAY 11
Comments
Kodi Episikopi amasankhidwa bwanji?

Kalata ya Dr. Saulos Klaus Chilima

Kalata ya Wachiwiri kwa Mtsogoleri wa dziko la Malawi, Dr. Saulos Klaus Chilima yodzudzula mchichitidwe woyambitsa ziwawa komanso kuwopsezana pa ndale.

44 MIN2018 MAY 11
Comments
Kalata ya Dr. Saulos Klaus Chilima

Kalata ya Aepiskopi Achikatolika M'malawi

Pologalamu yapadera yosimba yotambasula tsatanetsatane wa Kalata ya Aepiskopi Achikatolika M'malawi yotchedwa KUFUNIKA KWA KUSINTHA ZINTHU NDI KUYAMBANSO MOYO WATSOPANO M'MALAWI. Kalatayi idasindikizidwa pa 29 April, 2018.

97 MIN2018 MAY 9

Nzotheka ndi Ambuye _ Rev. Fr. Peter Mkhwayi

Bambo Peter Mkhwayi anachita ngozi yoopsa ya galimoto pa 01 October 2016 mpaka kuduka mkono wakumanja. Kodi anamva bwanji mmoyo wao atazindikira kuti mkono umodzi waduka. Kodi moyo wao wachikhulupiro unagwedezeka bwanji?

74 MIN2017 OCT 4

Tikuziona Bwanji Zovinavina pa Chipembedzo

Bambo Enock Kanjira kuyankha funso loti TIKUZIONA BWANJI ZOVINAVINA PACHIPEMBEDZO. Bambo Enock Kanjira ndi Mphunzitsi wamkulu ku seminary yaikulu ku Mchinji. Iwo adachita maphunziro aakulu okhudza chipembedzo kulikulu la mpingo ku Roma.

66 MIN2017 MAR 29

Ulaliki wa Ulemelero wa Pansi Pano_Bambo Joseph Kimu

Kodi nzoona kutu Ulaliki wa ulemelero wapansi pano ukupangitsa anthu ambiri mu Africa muno kukhala anthu osauka? Nanga inuyo mukamapita ku mpingo kwanu mumapita ndi zolinga ziti?Kukapeza chipulumutso kapena kukapeza chuma cha pansi pompano ndi zina Bambo Joseph Kimu ndi Funghai Mutsinze kukambirana za zotsatira za ulaliki umene umalonjeza anthu ulemelero wa pompopompo kapena kuti Gospel of Prosperity.

69 MIN2017 MAR 29

Tiphunzitseni Kupemphera

Pologamu ya padera ndi Bambo Elizeo Nthalika yokhudza buku lomwe alemba lotchedwa Tiphunzitseni Kupemphera.

69 MIN2017 MAR 23
Comments
Tiphunzitseni Kupemphera

Chikondi Cha Mulungu Chilibe Malire; Sister Agnes Chimbayo

Sister Agnes Chimbayo omwe amatumikira ku California ku United States of America kuphunzitsa za CHIKONDI CHA MULUNGU CHILIBE MALIRE

51 MIN2017 MAR 16

Pologalamu yapadera ndi Ambuye Montfort Stima Episkopi wa Dayosizi ya Mangochi

Pologalamu yapadera m'mene BamboJoseph Kimu akucheza ndi Ambuye Montfort Sitima, Episkopi wa dayosezi ya Mangochi pa kalata imene iwo alembera akhristu a dayosezi yawo pa nyengo ino ya Lenti.

69 MIN2017 MAR 12

Malawians in Dubai

Amalawi omwe akugwira ntchito ku United Arab Emirates (UAE) anali ndi msonkhano komanso nkumano ndi kuchita masewera amitundumitundi ndi cholinga cholimbikitsa umodzi wa a Malawi mu liyenda. Bambo Joseph Kimu anacheza ndi mmodzi wa a Malawi amene akukhala ku United Arab Emirates kuti adziwe kuti zinatheka bwanji kuchita dongosolo la mtunduli.

28 MIN2017 MAR 10