title

Tisanthule Baibulo @ ttb.twr.org/chichewa

Thru the Bible Chichewa

0
Followers
0
Plays

OVERVIEWEPISODESYOU MAY ALSO LIKE

Details

About Us

Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera pologalamu imodzi patsiku kuyambira lolemba mpaka lachisanu. Ngati mungakwanitse kutsatira ndondomekoyi, pakutha kwa zaka zisanu mudzakhala kuti mwawerenga Baibulo lonse.

Latest Episodes

Chikhulupiriro cha Rahabi ndi ena.

26 MIN1 d ago
Comments
Chikhulupiriro cha Rahabi ndi ena.

Chikhulupiriro cha Isake, Yakobo, Yosefe, Mose ndi Yoswa

26 MIN2 d ago

Chikhulupiriro cha Abraham ndi Sara

26 MIN3 d ago
Comments
Chikhulupiriro cha Abraham ndi Sara

Kukhulupirira Kristu kumadza ndi ntchito zabwino monga mwa chikhulupiriro cha Enoke ndi Nowa.

26 MIN6 d ago

Kuika chikhulupiriro mwa Kristu kumadza ndi ntchito komanso zinthu zabwino monga mwa chikhulupiriro cha Abele.

26 MIN1 w ago

Mwachikhulupiriro mwa Kristu, tipeza zabwino zonse ndi kuchita ntchito zabwino

Tsoka pakunyoza imfa ya Kristu

27 MIN1 w ago
Comments
Tsoka pakunyoza imfa ya Kristu

Kulimbika chifukwa cha Kristu amene ndinsembe yokwanira

Kristu ndiye Nsembe yoposa nsembe zonse

26 MIN1 w ago
Comments
Kristu ndiye Nsembe yoposa nsembe zonse

Kristu ndiye Nsembe yoposa zonse

27 MIN2 w ago

hmly
himalayaプレミアムへようこそ聴き放題のオーディオブックをお楽しみください。